Letra em Música Gerador de Letras Removedor de voz Preços Minhas Músicas App

Ndinali ndani

Song generated By ✨LyricsintoSong.com

Song Cover
v5 Lite

@ Jose Alberto Paulo

2026-11-15 17:06:39

Letras

[Instrumental hard Isigija from Botswana high light log drum]


[Intro, joyful heavy isigija, light log drum]
Ndinali ndani ine, kuti undikonde

[Instrumental hard Isigija high light log drum]


[Verse 1, joyful heay isigija, soft logdrum]
Ndinkayenda ndekha, ndilibe kopita
Moyo unali wovuta, ndikangoti bola kwacha
Anthu ankandinyoza, ankandiseka
Koma iwe unabwera, unandigwira dzanja

[Instrumental hard Isigija from Botswana high light log drum]


[Chorus, joyful isigija, high soft log drum louder, dancing]
Ndinali ndani ine, iwe wandikonda
Ndili osowa, iwe wandikonda
Ndinali wopanda kanthu, koma unandikondabe
Ndinali ndani ine, kuti undisunge

[Instrumental hard Isigija high light log drum]


[Verse 2, joyful isigija, high qualitylogdrum]
Tsopano ndili nawe, mtima wakhazikika
Maso ako akandiyang'ana, ndimayiwala zonse
Chikondi chako chandimanga, sindikuchoka
Wokondedwa wanga, ndiwe moyo wanga

[Instrumental hard Isigija heavy high light log drum]


[Chorus, joyful isigija, high soft log drum louder, dancing]
Ndinali ndani ine, iwe wandikonda
Ndili osowa, iwe wandikonda
Ndinali wopanda kanthu, koma unandikondabe
Ndinali ndani ine, kuti undisunge

[Instrumental heavy Isigija high light log drum]


[Outro, joyful isigija, heavylogdrum hitting hard]
Ndinali ndani ine, Zikomo wokondedwa

Estilo de Música

Joyful Isigija from Botswana, secular, romantic love song, mid-tempo, happy, danceable, groovy Botswana log drum, steady Botswana isigija beat, medium pace, not too fast, not too slow, verse and chorus, sweet, loving, celebratory, heartfelt, Male Vocals